Levitiko 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Musamapezeke munthu wina mu chihema chokumanako kuyambira pamene iye walowa m’malo oyera kukaphimba machimo kufikira atatulukamo. Ndipo aziphimba machimo ake,+ a nyumba yake ndi a mpingo wonse wa Isiraeli.+
17 “Musamapezeke munthu wina mu chihema chokumanako kuyambira pamene iye walowa m’malo oyera kukaphimba machimo kufikira atatulukamo. Ndipo aziphimba machimo ake,+ a nyumba yake ndi a mpingo wonse wa Isiraeli.+