Levitiko 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Usavule mlongo wako, mwana wamkazi wa bambo ako kapena mwana wamkazi wa mayi ako, kaya wobadwa naye m’banja limodzi kapena wobadwira m’banja lina, usawavule.+
9 “‘Usavule mlongo wako, mwana wamkazi wa bambo ako kapena mwana wamkazi wa mayi ako, kaya wobadwa naye m’banja limodzi kapena wobadwira m’banja lina, usawavule.+