Levitiko 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+
3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+