Levitiko 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 pamenepo ineyo ndidzam’kana munthu ameneyo pamodzi ndi banja lake,+ ndipo ndidzamupha pamodzi ndi onse ogwirizana naye pochita chiwerewere+ ndi Moleki, kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.
5 pamenepo ineyo ndidzam’kana munthu ameneyo pamodzi ndi banja lake,+ ndipo ndidzamupha pamodzi ndi onse ogwirizana naye pochita chiwerewere+ ndi Moleki, kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.