Levitiko 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma asayandikire nsalu yotchinga+ ndiponso guwa lansembe,+ chifukwa iye ali ndi chilema.+ Asaipitse malo anga opatulika,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikuwapatula kuti akhale oyera.’”+
23 Koma asayandikire nsalu yotchinga+ ndiponso guwa lansembe,+ chifukwa iye ali ndi chilema.+ Asaipitse malo anga opatulika,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikuwapatula kuti akhale oyera.’”+