Levitiko 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Chotero azisunga malamulo anga kuti asasenze tchimo ndi kufa,+ chifukwa chosasunga malamulowo ndi kuipitsa zinthu zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndawapatula monga anthu oyera.
9 “‘Chotero azisunga malamulo anga kuti asasenze tchimo ndi kufa,+ chifukwa chosasunga malamulowo ndi kuipitsa zinthu zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndawapatula monga anthu oyera.