Levitiko 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pa tsiku limeneli musagwire ntchito iliyonse, chifukwa ndi tsiku lochita mwambo wophimba machimo+ anu pamaso pa Yehova Mulungu wanu.
28 Pa tsiku limeneli musagwire ntchito iliyonse, chifukwa ndi tsiku lochita mwambo wophimba machimo+ anu pamaso pa Yehova Mulungu wanu.