Levitiko 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mnyamatayo anayamba kunyoza ndi kutukwana+ dzina la Mulungu.+ Chotero anabwera naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri, wa fuko la Dani.
11 Kenako mnyamatayo anayamba kunyoza ndi kutukwana+ dzina la Mulungu.+ Chotero anabwera naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri, wa fuko la Dani.