-
Levitiko 25:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndipo inuyo, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, waganyu wanu, mlendo wokhaliratu amene akukhala pakati panu, ndi alendo ena okhala m’nyumba mwanu, muzidya zimene zamera m’chaka cha sabatacho.
-