Numeri 4:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Amenewa ndiwo anawerengedwa mwa mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera mawu a Yehova kwa Mose.+
45 Amenewa ndiwo anawerengedwa mwa mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera mawu a Yehova kwa Mose.+