Numeri 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Masiku onse a lonjezo lake lokhala Mnaziri, lezala lisadutse kumutu kwake+ kufikira atatha masiku ake amene anadzipereka kwa Yehova. Azikhala woyera mwa kusiya tsitsi+ lake la kumutu kuti likule.
5 “‘Masiku onse a lonjezo lake lokhala Mnaziri, lezala lisadutse kumutu kwake+ kufikira atatha masiku ake amene anadzipereka kwa Yehova. Azikhala woyera mwa kusiya tsitsi+ lake la kumutu kuti likule.