Numeri 7:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Komanso anapereka ng’ombe yaing’ono yamphongo imodzi, nkhosa imodzi yamphongo, ndi mwana wa nkhosa wamphongo wosapitirira chaka chimodzi. Nyama zimenezi zinali za nsembe yopsereza.+
45 Komanso anapereka ng’ombe yaing’ono yamphongo imodzi, nkhosa imodzi yamphongo, ndi mwana wa nkhosa wamphongo wosapitirira chaka chimodzi. Nyama zimenezi zinali za nsembe yopsereza.+