Numeri 7:86 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 86 Anaperekanso zikho 12 zagolide+ zodzaza ndi zofukiza. Chikho chilichonse chinali cholemera masekeli 10, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Golide yense wa zikho zonsezi anali wolemera masekeli 120.
86 Anaperekanso zikho 12 zagolide+ zodzaza ndi zofukiza. Chikho chilichonse chinali cholemera masekeli 10, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Golide yense wa zikho zonsezi anali wolemera masekeli 120.