Numeri 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pambuyo pake, Aleviwo azitumikira pachihema chokumanako.+ Chotero uwayeretse, ndi kuwauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula.+
15 Pambuyo pake, Aleviwo azitumikira pachihema chokumanako.+ Chotero uwayeretse, ndi kuwauza kuti ayende uku ndi uku monga nsembe yoweyula.+