Numeri 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano anthuwo anayamba kudandaula pamaso pa Yehova ngati kuti anali pamavuto.+ Yehova atamva kudandaulako anawapsera mtima, ndipo moto wa Yehova unawayakira n’kupsereza ena a iwo kumalire a msasa.+
11 Tsopano anthuwo anayamba kudandaula pamaso pa Yehova ngati kuti anali pamavuto.+ Yehova atamva kudandaulako anawapsera mtima, ndipo moto wa Yehova unawayakira n’kupsereza ena a iwo kumalire a msasa.+