Numeri 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngakhale zili choncho, anthu okhala kumeneko ndi anthu amphamvu zawo, mizinda yawo ndi yotchingidwa ndi mipanda yolimba kwambiri ndiponso yaitali.+ Si zokhazo, mbadwa za Anaki zija tinaziona kumeneko.+
28 Ngakhale zili choncho, anthu okhala kumeneko ndi anthu amphamvu zawo, mizinda yawo ndi yotchingidwa ndi mipanda yolimba kwambiri ndiponso yaitali.+ Si zokhazo, mbadwa za Anaki zija tinaziona kumeneko.+