Numeri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zimene mukuchitazi, iweyo limodzi ndi khamu lako lonseli, mukuukira Yehova.+ Kunena za Aroni, kodi iye ndani kuti amuna inu mum’dandaule?”+
11 Zimene mukuchitazi, iweyo limodzi ndi khamu lako lonseli, mukuukira Yehova.+ Kunena za Aroni, kodi iye ndani kuti amuna inu mum’dandaule?”+