18 Ndiyeno munthu wosadetsedwa+ atenge kamtengo ka hisope.+ Akaviike m’madziwo n’kuwaza hemalo. Awazenso ziwiya zonse ndi anthu onse amene anali muhemalo. Komanso, awaze munthu amene anakhudza fupa la munthu, kapena kukhudza munthu wophedwa, kapenanso mtembo uliwonse, ngakhalenso manda a munthu.