Numeri 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa iwo, kuti munthu wowaza madzi oyeretsera, komanso munthu amene angakhudze madziwo, azichapa zovala zake.+ Akatero, azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.
21 “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa iwo, kuti munthu wowaza madzi oyeretsera, komanso munthu amene angakhudze madziwo, azichapa zovala zake.+ Akatero, azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.