Numeri 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Isiraeliwo anayankha kuti: “Ife tidzangodutsa mumsewu waukulu, ndipo ngati tidzamwa madzi anu, ife kapena ziweto zathu, ndithu tidzalipira mtengo wake.+ Sitikufuna chilichonse ayi, koma kungodutsa m’dziko lanu basi.”+
19 Ana a Isiraeliwo anayankha kuti: “Ife tidzangodutsa mumsewu waukulu, ndipo ngati tidzamwa madzi anu, ife kapena ziweto zathu, ndithu tidzalipira mtengo wake.+ Sitikufuna chilichonse ayi, koma kungodutsa m’dziko lanu basi.”+