-
Numeri 23:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Balamu atabwerera kwa Balaki, anam’peza ataima pafupi ndi nsembe yake yopsereza, akalonga a ku Mowabu ali naye limodzi pamenepo. Ndiyeno Balaki anafunsa Balamu kuti: “Kodi Yehova wati chiyani?”
-