Numeri 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mawu a iye wakumva zonena za Mulungu,+Iye amene waona masomphenya a Wamphamvuyonse,+Pamene anali kugwa pansi, maso ake ali chipenyere.+ Mawu ake akuti:
4 Mawu a iye wakumva zonena za Mulungu,+Iye amene waona masomphenya a Wamphamvuyonse,+Pamene anali kugwa pansi, maso ake ali chipenyere.+ Mawu ake akuti: