Numeri 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anayambanso kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti:“Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna wamphamvu, maso ake ali chitsegukire,+
15 Kenako anayambanso kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti:“Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna wamphamvu, maso ake ali chitsegukire,+