Numeri 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu a munthu womva zonena za Mulungu,+Iye wozindikira nzeru za Wam’mwambamwamba . . .Iye anaona masomphenya a Wamphamvuyonse+Pamene anali kugwa pansi, maso ake ali chipenyere.+ Mawu ake ndi akuti:
16 Mawu a munthu womva zonena za Mulungu,+Iye wozindikira nzeru za Wam’mwambamwamba . . .Iye anaona masomphenya a Wamphamvuyonse+Pamene anali kugwa pansi, maso ake ali chipenyere.+ Mawu ake ndi akuti: