18 chifukwa akubweretserani tsoka mochenjera,+ pokukopani kuti muchimwe ku Peori.+ Muwakanthe ndithu, chifukwanso cha zochita za mlongo wawo Kozibi,+ mwana wa mtsogoleri wa ku Midiyani, amene anaphedwa+ pa tsiku limene mliri unakugwerani chifukwa cha zimene zinachitika ku Peori.”+