Numeri 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Um’patseko ulemerero wako,+ kuti khamu lonse la ana a Isiraeli lizimumvera.+