Numeri 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye anawauza kuti: “Ana a Gadi ndi ana a Rubeni akawoloka nanu Yorodano, aliyense wokonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, ndipo ngati dzikolo lidzagonjetsedwa pamaso panu, pamenepo mudzawapatse dziko la Giliyadi monga cholowa chawo.+
29 Iye anawauza kuti: “Ana a Gadi ndi ana a Rubeni akawoloka nanu Yorodano, aliyense wokonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, ndipo ngati dzikolo lidzagonjetsedwa pamaso panu, pamenepo mudzawapatse dziko la Giliyadi monga cholowa chawo.+