Numeri 33:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Tsopano mfumu ina yachikanani, mfumu ya Aradi,+ imene inali kukhala ku Negebu+ m’dziko la kanani, inamva kuti ana a Isiraeli akubwera.
40 Tsopano mfumu ina yachikanani, mfumu ya Aradi,+ imene inali kukhala ku Negebu+ m’dziko la kanani, inamva kuti ana a Isiraeli akubwera.