Numeri 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero Mose anauza ana a Isiraeli kuti: “Ili ndilo dziko limene ligawidwe kwa inu mwa maere+ monga cholowa chanu. Lidzagawidwa kwa inu monga momwe Yehova analamulira kuti lipatsidwe kwa mafuko 9 ndi hafu.+
13 Chotero Mose anauza ana a Isiraeli kuti: “Ili ndilo dziko limene ligawidwe kwa inu mwa maere+ monga cholowa chanu. Lidzagawidwa kwa inu monga momwe Yehova analamulira kuti lipatsidwe kwa mafuko 9 ndi hafu.+