Deuteronomo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Mwayenda kwa nthawi yaitali m’dera lapafupi ndi phirili.+ Tembenukani ndi kulowera kumpoto.