Deuteronomo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Dzanja+ la Yehova linali pa iwo kuwasautsa ndi kuwachotsa pakati panu, kufikira onse atatha.+