Deuteronomo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+
3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+