Deuteronomo 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ndipo Yehova anandikwiyira chifukwa cha inu,+ kotero kuti analumbira kuti ndisawoloke Yorodano, kapena kulowa m’dziko labwino limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala cholowa chanu.+
21 “Ndipo Yehova anandikwiyira chifukwa cha inu,+ kotero kuti analumbira kuti ndisawoloke Yorodano, kapena kulowa m’dziko labwino limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala cholowa chanu.+