Deuteronomo 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+
24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+