Deuteronomo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ monga mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira, kuti masiku ako atalike, ndi kuti zinthu zikuyendere bwino+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.
16 “‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ monga mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira, kuti masiku ako atalike, ndi kuti zinthu zikuyendere bwino+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.