Deuteronomo 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iwe ima pompano, ndipo ndikuuza malamulo onse, malangizo ndi zigamulo zimene uyenera kuwaphunzitsa+ kuti azikazitsatira m’dziko limene ndikuwapatsa kukhala lawo.’
31 Koma iwe ima pompano, ndipo ndikuuza malamulo onse, malangizo ndi zigamulo zimene uyenera kuwaphunzitsa+ kuti azikazitsatira m’dziko limene ndikuwapatsa kukhala lawo.’