12 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Nyamuka, tsika mofulumira m’phiri muno, chifukwa anthu ako amene unawatulutsa ku Iguputo achita zinthu zowawonongetsa.+ Apatuka mofulumira panjira imene ndinawalamula kuyendamo. Adzipangira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.’+