Deuteronomo 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Chotero ndinadzigwetsa pansi pamaso pa Yehova masiku 40, usana ndi usiku.+ Ndinadzigwetsa choncho chifukwa Yehova anati akufuna kukufafanizani.+
25 “Chotero ndinadzigwetsa pansi pamaso pa Yehova masiku 40, usana ndi usiku.+ Ndinadzigwetsa choncho chifukwa Yehova anati akufuna kukufafanizani.+