Deuteronomo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ndinapanga likasa la mtengo wa mthethe ndi kusema miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija.+ Kenako ndinakwera m’phiri, miyala iwiriyo ili m’manja mwanga.
3 Choncho ndinapanga likasa la mtengo wa mthethe ndi kusema miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija.+ Kenako ndinakwera m’phiri, miyala iwiriyo ili m’manja mwanga.