Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Nsanja ya Olonda,9/15/2004, tsa. 27
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa.