Deuteronomo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chaka ndi chaka iweyo ndi banja lako muzidya mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe kapena wa nkhosa pamaso pa Yehova Mulungu wako, pamalo amene Yehova adzasankhe.+
20 Chaka ndi chaka iweyo ndi banja lako muzidya mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe kapena wa nkhosa pamaso pa Yehova Mulungu wako, pamalo amene Yehova adzasankhe.+