Deuteronomo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+
25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+