Deuteronomo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo akulu a mzindawo amuitane ndi kulankhula naye. Iye aime pamaso pawo ndi kunena kuti, ‘Sindikufuna kutenga mkazi ameneyu.’+
8 Pamenepo akulu a mzindawo amuitane ndi kulankhula naye. Iye aime pamaso pawo ndi kunena kuti, ‘Sindikufuna kutenga mkazi ameneyu.’+