Deuteronomo 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ng’ombe yako idzaphedwa iwe ukuona, koma nyama yake sudzadyako. Bulu wako adzalandidwa ndi achifwamba iwe ukuona, ndipo sudzamuonanso. Nkhosa yako idzaperekedwa kwa adani ako, koma sipadzakhala wokupulumutsa.+
31 Ng’ombe yako idzaphedwa iwe ukuona, koma nyama yake sudzadyako. Bulu wako adzalandidwa ndi achifwamba iwe ukuona, ndipo sudzamuonanso. Nkhosa yako idzaperekedwa kwa adani ako, koma sipadzakhala wokupulumutsa.+