Deuteronomo 28:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:45 Nsanja ya Olonda,1/15/1995, ptsa. 15-16
45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+