Yoswa 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’”
3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’”