Yoswa 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku 7, anadzuka m’mawa kutangoyamba kucha, ndipo anaguba kuzungulira mzindawo monga anali kuchitira. Pa tsiku la 7 limeneli, anazungulira mzindawo maulendo 7.+
15 Pa tsiku 7, anadzuka m’mawa kutangoyamba kucha, ndipo anaguba kuzungulira mzindawo monga anali kuchitira. Pa tsiku la 7 limeneli, anazungulira mzindawo maulendo 7.+