Yoswa 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo Rahabi hule uja, limodzi ndi anthu a m’nyumba ya bambo ake, ndi onse amene anali naye, Yoswa sanawaphe.+ Kufikira lero, mayiyo akukhalabe pakati pa Aisiraeli,+ chifukwa anabisa anyamata amene Yoswa anawatuma kukazonda Yeriko.+
25 Ndipo Rahabi hule uja, limodzi ndi anthu a m’nyumba ya bambo ake, ndi onse amene anali naye, Yoswa sanawaphe.+ Kufikira lero, mayiyo akukhalabe pakati pa Aisiraeli,+ chifukwa anabisa anyamata amene Yoswa anawatuma kukazonda Yeriko.+