Yoswa 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anapita kwa Yoswa kumsasa wa ku Giligala,+ ndipo anauza iye ndi amuna achiisiraeli kuti: “Ife tachokera kudziko lakutali kwambiri. Chonde, chitani nafe pangano.”+
6 Kenako anapita kwa Yoswa kumsasa wa ku Giligala,+ ndipo anauza iye ndi amuna achiisiraeli kuti: “Ife tachokera kudziko lakutali kwambiri. Chonde, chitani nafe pangano.”+