Yoswa 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anamuyankha kuti: “Akapolo anufe tachokera kudziko lakutali kwambiri.+ Tabwera chifukwa tamva za dzina+ la Mulungu wanu, Yehova. Tamva mbiri yake ndi zonse zimene anachita ku Iguputo.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Nsanja ya Olonda,10/15/2004, tsa. 18
9 Iwo anamuyankha kuti: “Akapolo anufe tachokera kudziko lakutali kwambiri.+ Tabwera chifukwa tamva za dzina+ la Mulungu wanu, Yehova. Tamva mbiri yake ndi zonse zimene anachita ku Iguputo.+